Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qamar ayat 25 - القَمَر - Page - Juz 27
﴿أَءُلۡقِيَ ٱلذِّكۡرُ عَلَيۡهِ مِنۢ بَيۡنِنَا بَلۡ هُوَ كَذَّابٌ أَشِرٞ ﴾ 
[القَمَر: 25]
﴿أؤلقي الذكر عليه من بيننا بل هو كذاب أشر﴾ [القَمَر: 25]
| Khaled Ibrahim Betala “Kodi am’vumbulutsira iye chikumbutso pakati pathu, (pomwe tili nawo oposa iye pa ulemelero)? Koma iye ndiwabodza ndi wodzitukumu.” |