Quran with Chichewa translation - Surah Al-Waqi‘ah ayat 89 - الوَاقِعة - Page - Juz 27
﴿فَرَوۡحٞ وَرَيۡحَانٞ وَجَنَّتُ نَعِيمٖ ﴾
[الوَاقِعة: 89]
﴿فروح وريحان وجنة نعيم﴾ [الوَاقِعة: 89]
Khaled Ibrahim Betala “Kobwerera kwake ndi kumpumulo ndi mtendere ndi kupatsidwa zonunkhira ndiponso Munda wamtendere |