Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 90 - الأنعَام - Page - Juz 7
﴿أُوْلَٰٓئِكَ ٱلَّذِينَ هَدَى ٱللَّهُۖ فَبِهُدَىٰهُمُ ٱقۡتَدِهۡۗ قُل لَّآ أَسۡـَٔلُكُمۡ عَلَيۡهِ أَجۡرًاۖ إِنۡ هُوَ إِلَّا ذِكۡرَىٰ لِلۡعَٰلَمِينَ ﴾
[الأنعَام: 90]
﴿أولئك الذين هدى الله فبهداهم اقتده قل لا أسألكم عليه أجرا إن﴾ [الأنعَام: 90]
Khaled Ibrahim Betala “Iwo ndi omwe Allah adawaongola choncho, tsatira chiongoko chawo. Nena: “Sindikukupemphani malipiro pa izi (zomwe ndikukuphunzitsanizi, koma ndikungotumikira Allah). Ichi sichina koma ndi ulaliki kwa zolengedwa (majini ndi anthu).” |