×

Mulungu wakulolezani kuti mukhoza kumasula malonjezo anu. Ndipo Mulungu ndiye Mtetezi wanu, 66:2 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Tahrim ⮕ (66:2) ayat 2 in Chichewa

66:2 Surah At-Tahrim ayat 2 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Tahrim ayat 2 - التَّحرِيم - Page - Juz 28

﴿قَدۡ فَرَضَ ٱللَّهُ لَكُمۡ تَحِلَّةَ أَيۡمَٰنِكُمۡۚ وَٱللَّهُ مَوۡلَىٰكُمۡۖ وَهُوَ ٱلۡعَلِيمُ ٱلۡحَكِيمُ ﴾
[التَّحرِيم: 2]

Mulungu wakulolezani kuti mukhoza kumasula malonjezo anu. Ndipo Mulungu ndiye Mtetezi wanu, ndipo ndi wodziwa ndi Mwini nzeru zonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قد فرض الله لكم تحلة أيمانكم والله مولاكم وهو العليم الحكيم, باللغة نيانجا

﴿قد فرض الله لكم تحلة أيمانكم والله مولاكم وهو العليم الحكيم﴾ [التَّحرِيم: 2]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu Allah wakhazikitsa kamasulidwe kakulumbira kwanu, ndipo Allah ndiye Mtetezi wanu, Iye Ngodziwa kwambiri ndiponso Ngwanzeru zakuya (pa malamulo amene wawakhazikitsa kwa inu)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek