Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qalam ayat 18 - القَلَم - Page - Juz 29
﴿وَلَا يَسۡتَثۡنُونَ ﴾
[القَلَم: 18]
﴿ولا يستثنون﴾ [القَلَم: 18]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo sadapatule (ngakhale wosauka ndi m’modzi yemwe ponena kuti uje timpatse, uje tisampatse, kapena sadanene kuti: “Ngati Allah afuna).” |