×

Nena, “Oh inu anthu! Ndithudi ine ndatumizidwa ngati Mtumwi wa Mulungu kwa 7:158 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:158) ayat 158 in Chichewa

7:158 Surah Al-A‘raf ayat 158 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 158 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿قُلۡ يَٰٓأَيُّهَا ٱلنَّاسُ إِنِّي رَسُولُ ٱللَّهِ إِلَيۡكُمۡ جَمِيعًا ٱلَّذِي لَهُۥ مُلۡكُ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِۖ لَآ إِلَٰهَ إِلَّا هُوَ يُحۡيِۦ وَيُمِيتُۖ فَـَٔامِنُواْ بِٱللَّهِ وَرَسُولِهِ ٱلنَّبِيِّ ٱلۡأُمِّيِّ ٱلَّذِي يُؤۡمِنُ بِٱللَّهِ وَكَلِمَٰتِهِۦ وَٱتَّبِعُوهُ لَعَلَّكُمۡ تَهۡتَدُونَ ﴾
[الأعرَاف: 158]

Nena, “Oh inu anthu! Ndithudi ine ndatumizidwa ngati Mtumwi wa Mulungu kwa inu nonse, yemwe ali Mwini ufumu wakumwamba ndi wa padziko lapansi. Kulibe mulungu wina koma Iye yekha. Iye amapereka moyo ndi imfa. Motero khulupilirani mwa Mulungu ndi mwa Mtumwi wake, Mtumwi yemwe sadziwa kuwerenga ndi kulemba, amene amakhulupirira mwa Mulungu ndi m’Mawu ake. Ndipo mutsatireni iye kuti mukhale otsogozedwa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل ياأيها الناس إني رسول الله إليكم جميعا الذي له ملك السموات, باللغة نيانجا

﴿قل ياأيها الناس إني رسول الله إليكم جميعا الذي له ملك السموات﴾ [الأعرَاف: 158]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “E inu anthu! Ndithu ine ndine Mtumiki wa Allah kwa inu nonse. (Allah) Yemwe ali nawo ufumu wa kumwamba ndi pansi. Palibe wopembedzedwa mwa choonadi koma Iye. Amapatsa moyo ndi imfa. Choncho, khulupirirani mwa Allah ndi Mtumiki Wake yemwe ndi Mneneri wosadziwa kulemba ndi kuwerenga, yemwe akukhulupirira Allah ndi mawu Ake. Ndipo mtsatireni kuti muongoke.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek