×

Nena, “Ambuye wanga adaletsa ntchito zonse zonyansa kaya zooneka poyera kapena zobisika, 7:33 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:33) ayat 33 in Chichewa

7:33 Surah Al-A‘raf ayat 33 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 33 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿قُلۡ إِنَّمَا حَرَّمَ رَبِّيَ ٱلۡفَوَٰحِشَ مَا ظَهَرَ مِنۡهَا وَمَا بَطَنَ وَٱلۡإِثۡمَ وَٱلۡبَغۡيَ بِغَيۡرِ ٱلۡحَقِّ وَأَن تُشۡرِكُواْ بِٱللَّهِ مَا لَمۡ يُنَزِّلۡ بِهِۦ سُلۡطَٰنٗا وَأَن تَقُولُواْ عَلَى ٱللَّهِ مَا لَا تَعۡلَمُونَ ﴾
[الأعرَاف: 33]

Nena, “Ambuye wanga adaletsa ntchito zonse zonyansa kaya zooneka poyera kapena zobisika, machimo, kuponderezana popanda chilungamo, kumphatikiza Mulungu ndi zimene sadalamulire ndi kunena za Mulungu zimene inu simuli kuzidziwa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل إنما حرم ربي الفواحش ما ظهر منها وما بطن والإثم والبغي, باللغة نيانجا

﴿قل إنما حرم ربي الفواحش ما ظهر منها وما بطن والإثم والبغي﴾ [الأعرَاف: 33]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena (kwa iwo): “Ndithu Mbuye wanga waletsa zinthu zauve zoonekera ndi zobisika, ndi machimo, ndi kuwukira (atsogoleri) popanda choonadi, ndi kumphatikiza Allah ndi chomwe sadachitsitsire umboni (wakuti chiphatikizidwe ndi Iye); ndiponso (waletsa) kumunenera Allah zimene simukuzidziwa.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek