×

Iwo adati: “Iwe wadza kuti ife tizingopembedza Mulungu yekha ndi kusiya milungu 7:70 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:70) ayat 70 in Chichewa

7:70 Surah Al-A‘raf ayat 70 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 70 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿قَالُوٓاْ أَجِئۡتَنَا لِنَعۡبُدَ ٱللَّهَ وَحۡدَهُۥ وَنَذَرَ مَا كَانَ يَعۡبُدُ ءَابَآؤُنَا فَأۡتِنَا بِمَا تَعِدُنَآ إِن كُنتَ مِنَ ٱلصَّٰدِقِينَ ﴾
[الأعرَاف: 70]

Iwo adati: “Iwe wadza kuti ife tizingopembedza Mulungu yekha ndi kusiya milungu imene makolo athu adali kupembedza. Motero bweretsa chimene ukutiopseza nacho ngati zimene uli kunena ndi zoona.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قالوا أجئتنا لنعبد الله وحده ونذر ما كان يعبد آباؤنا فأتنا بما, باللغة نيانجا

﴿قالوا أجئتنا لنعبد الله وحده ونذر ما كان يعبد آباؤنا فأتنا بما﴾ [الأعرَاف: 70]

Khaled Ibrahim Betala
“Iwo adati: “Kodi watidzera kuti timpembedze Allah Yekha ndikusiya zomwe ankapembedza makolo athu? Tibweretsere chimene ukutilonjezacho ngati uli mmodzi mwa onena zoona.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek