Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jinn ayat 4 - الجِن - Page - Juz 29
﴿وَأَنَّهُۥ كَانَ يَقُولُ سَفِيهُنَا عَلَى ٱللَّهِ شَطَطٗا ﴾
[الجِن: 4]
﴿وأنه كان يقول سفيهنا على الله شططا﴾ [الجِن: 4]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ndithu mbuli za mwa ife zakhala zikunenera Allah mawu abodza (okhala kutali ndi choonadi) |