Quran with Chichewa translation - Surah An-Naba’ ayat 37 - النَّبَإ - Page - Juz 30
﴿رَّبِّ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِ وَمَا بَيۡنَهُمَا ٱلرَّحۡمَٰنِۖ لَا يَمۡلِكُونَ مِنۡهُ خِطَابٗا ﴾
[النَّبَإ: 37]
﴿رب السموات والأرض وما بينهما الرحمن لا يملكون منه خطابا﴾ [النَّبَإ: 37]
Khaled Ibrahim Betala “Mbuye wa kumwamba ndi pansi ndi zimene zili pakati pake; Wachifundo chambiri. Palibe amene adzakhala ndi mphamvu yolankhulana naye (pa tsiku limenero) |