×

Ndi kuchotsa mkwiyo m’mitima mwawo. Mulungu amakhululukira aliyense amene Iye wamufuna. Mulungu 9:15 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:15) ayat 15 in Chichewa

9:15 Surah At-Taubah ayat 15 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 15 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿وَيُذۡهِبۡ غَيۡظَ قُلُوبِهِمۡۗ وَيَتُوبُ ٱللَّهُ عَلَىٰ مَن يَشَآءُۗ وَٱللَّهُ عَلِيمٌ حَكِيمٌ ﴾
[التوبَة: 15]

Ndi kuchotsa mkwiyo m’mitima mwawo. Mulungu amakhululukira aliyense amene Iye wamufuna. Mulungu ndi wodziwa ndipo ndi wanzeru

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ويذهب غيظ قلوبهم ويتوب الله على من يشاء والله عليم حكيم, باللغة نيانجا

﴿ويذهب غيظ قلوبهم ويتوب الله على من يشاء والله عليم حكيم﴾ [التوبَة: 15]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndi kuchotsa mkwiyo wa m’mitima mwawo (Asilamu). Ndi kuti Allah Alandire kulapa kwa amene wamfuna. Ndipo Allah Ngodziwa, Ngwanzeru zakuya
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek