×

Iwo amene adakhulupirira, nasamuka, ndipo analimbikira m’njira ya Mulungu ndi chuma chawo 9:20 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:20) ayat 20 in Chichewa

9:20 Surah At-Taubah ayat 20 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 20 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَهَاجَرُواْ وَجَٰهَدُواْ فِي سَبِيلِ ٱللَّهِ بِأَمۡوَٰلِهِمۡ وَأَنفُسِهِمۡ أَعۡظَمُ دَرَجَةً عِندَ ٱللَّهِۚ وَأُوْلَٰٓئِكَ هُمُ ٱلۡفَآئِزُونَ ﴾
[التوبَة: 20]

Iwo amene adakhulupirira, nasamuka, ndipo analimbikira m’njira ya Mulungu ndi chuma chawo pamodzi ndi iwo eni, iwo ali ndi udindo waukulu pamaso pa Mulungu. Iwo ndiwo opambana

❮ Previous Next ❯

ترجمة: الذين آمنوا وهاجروا وجاهدوا في سبيل الله بأموالهم وأنفسهم أعظم درجة عند, باللغة نيانجا

﴿الذين آمنوا وهاجروا وجاهدوا في سبيل الله بأموالهم وأنفسهم أعظم درجة عند﴾ [التوبَة: 20]

Khaled Ibrahim Betala
“Amene akhulupirira, ndi kusamuka, ndi kumenya nkhondo pa njira ya Allah ndi chuma chawo ndi matupi awo, ali ndi ulemelero waukulu kwa Allah. Iwowo ndiwo opambana
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek