Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 21 - التوبَة - Page - Juz 10
﴿يُبَشِّرُهُمۡ رَبُّهُم بِرَحۡمَةٖ مِّنۡهُ وَرِضۡوَٰنٖ وَجَنَّٰتٖ لَّهُمۡ فِيهَا نَعِيمٞ مُّقِيمٌ ﴾
[التوبَة: 21]
﴿يبشرهم ربهم برحمة منه ورضوان وجنات لهم فيها نعيم مقيم﴾ [التوبَة: 21]
Khaled Ibrahim Betala “Mbuye wawo akuwauza nkhani yabwino ya chifundo chochokera kwa Iye, ndi chiyanjo (Chake) ndi Minda yomwe mkati mwake adzapezamo mtendere wamuyaya |