Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 29 - التوبَة - Page - Juz 10
﴿قَٰتِلُواْ ٱلَّذِينَ لَا يُؤۡمِنُونَ بِٱللَّهِ وَلَا بِٱلۡيَوۡمِ ٱلۡأٓخِرِ وَلَا يُحَرِّمُونَ مَا حَرَّمَ ٱللَّهُ وَرَسُولُهُۥ وَلَا يَدِينُونَ دِينَ ٱلۡحَقِّ مِنَ ٱلَّذِينَ أُوتُواْ ٱلۡكِتَٰبَ حَتَّىٰ يُعۡطُواْ ٱلۡجِزۡيَةَ عَن يَدٖ وَهُمۡ صَٰغِرُونَ ﴾
[التوبَة: 29]
﴿قاتلوا الذين لا يؤمنون بالله ولا باليوم الآخر ولا يحرمون ما حرم﴾ [التوبَة: 29]
Khaled Ibrahim Betala “Menyanani ndi omwe sakhulupirira Allah ndi tsiku lachimaliziro, omwenso sakusiya zoletsedwa zomwe Allah ndi Mtumiki Wake waletsa; omwenso satsatira chipembedzo choona mwa amene adapatsidwa mabuku. (Menyanani nawo) kufikira apereke msonkho ndi manja awo uku ali odzichepetsa |