Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 30 - التوبَة - Page - Juz 10
﴿وَقَالَتِ ٱلۡيَهُودُ عُزَيۡرٌ ٱبۡنُ ٱللَّهِ وَقَالَتِ ٱلنَّصَٰرَى ٱلۡمَسِيحُ ٱبۡنُ ٱللَّهِۖ ذَٰلِكَ قَوۡلُهُم بِأَفۡوَٰهِهِمۡۖ يُضَٰهِـُٔونَ قَوۡلَ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ مِن قَبۡلُۚ قَٰتَلَهُمُ ٱللَّهُۖ أَنَّىٰ يُؤۡفَكُونَ ﴾
[التوبَة: 30]
﴿وقالت اليهود عزير ابن الله وقالت النصارى المسيح ابن الله ذلك قولهم﴾ [التوبَة: 30]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo Ayuda akunena kuti Uzairi ndimwana wa Mulungu, naonso Akhrisitu akunena kuti Mesiya (Isa {Yesu}) ndimwana wa Mulungu. Awa ndi mawu amene akunena ndi pakamwa pawo (popanda umboni wochokera kwa Allah); akutsanzira zonena za omwe sadakhulupirire kale. Allah awaononge; kodi iwo akusokera chotani (kusiya choonadi) |