×

oh inu anthu okhulupirira! Ndithudi anthu opembedza mafano ndi uve. Motero asayandikire 9:28 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:28) ayat 28 in Chichewa

9:28 Surah At-Taubah ayat 28 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 28 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُوٓاْ إِنَّمَا ٱلۡمُشۡرِكُونَ نَجَسٞ فَلَا يَقۡرَبُواْ ٱلۡمَسۡجِدَ ٱلۡحَرَامَ بَعۡدَ عَامِهِمۡ هَٰذَاۚ وَإِنۡ خِفۡتُمۡ عَيۡلَةٗ فَسَوۡفَ يُغۡنِيكُمُ ٱللَّهُ مِن فَضۡلِهِۦٓ إِن شَآءَۚ إِنَّ ٱللَّهَ عَلِيمٌ حَكِيمٞ ﴾
[التوبَة: 28]

oh inu anthu okhulupirira! Ndithudi anthu opembedza mafano ndi uve. Motero asayandikire pafupi ndi Mzikiti Wolemekezeka chikatha chaka chino ndipo ngati inu muopa umphawi, Mulungu, ngati afuna, adzakulemeretsani inu kuchokera ku chuma chake. Ndithudi Mulungu amadziwa chilichonse ndipo ndi Wanzeru

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها الذين آمنوا إنما المشركون نجس فلا يقربوا المسجد الحرام بعد عامهم, باللغة نيانجا

﴿ياأيها الذين آمنوا إنما المشركون نجس فلا يقربوا المسجد الحرام بعد عامهم﴾ [التوبَة: 28]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu amene mwakhulupirira! Ndithu opembedza mafano ndi nyansi, choncho, asayandikire Msikiti Wopatulika chikatha chaka chaochi. Ngati mukuopa umphawi, posachedwa Allah Akulemeretsani ndi zabwino Zake akafuna. Ndithu Allah Ngodziwa zonse, Ngwanzeru zakuya
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek