×

Iye ndiye amene adatumiza Mtumwi wake ndi chilangizo ndi chipembedzo choonadi kuti 9:33 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:33) ayat 33 in Chichewa

9:33 Surah At-Taubah ayat 33 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 33 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿هُوَ ٱلَّذِيٓ أَرۡسَلَ رَسُولَهُۥ بِٱلۡهُدَىٰ وَدِينِ ٱلۡحَقِّ لِيُظۡهِرَهُۥ عَلَى ٱلدِّينِ كُلِّهِۦ وَلَوۡ كَرِهَ ٱلۡمُشۡرِكُونَ ﴾
[التوبَة: 33]

Iye ndiye amene adatumiza Mtumwi wake ndi chilangizo ndi chipembedzo choonadi kuti chipambane zipembedzo zina zonse ngakhale kuti anthu opembedza mafano amadana nazo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: هو الذي أرسل رسوله بالهدى ودين الحق ليظهره على الدين كله ولو, باللغة نيانجا

﴿هو الذي أرسل رسوله بالهدى ودين الحق ليظهره على الدين كله ولو﴾ [التوبَة: 33]

Khaled Ibrahim Betala
“Iye ndi Yemwe adatuma Mtumiki Wake ndi ulangizi ndiponso chipembedzo choona kuti achiwonetsere pa zipembedzo zonse, ngakhale atanyansidwa nazo Amushirikina
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek