×

Kupatula opembedza mafano amene mwapangana nawo chipangano, ndipo sadakukhumudwitseni pa chilichonse ndipo 9:4 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:4) ayat 4 in Chichewa

9:4 Surah At-Taubah ayat 4 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 4 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿إِلَّا ٱلَّذِينَ عَٰهَدتُّم مِّنَ ٱلۡمُشۡرِكِينَ ثُمَّ لَمۡ يَنقُصُوكُمۡ شَيۡـٔٗا وَلَمۡ يُظَٰهِرُواْ عَلَيۡكُمۡ أَحَدٗا فَأَتِمُّوٓاْ إِلَيۡهِمۡ عَهۡدَهُمۡ إِلَىٰ مُدَّتِهِمۡۚ إِنَّ ٱللَّهَ يُحِبُّ ٱلۡمُتَّقِينَ ﴾
[التوبَة: 4]

Kupatula opembedza mafano amene mwapangana nawo chipangano, ndipo sadakukhumudwitseni pa chilichonse ndipo sadamthandize aliyense kulimbana ndi inu. Kotero kwaniritsani chipangano chawo kufikira kunthawi yawo. Ndithudi Mulungu amakonda amene amaopa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إلا الذين عاهدتم من المشركين ثم لم ينقصوكم شيئا ولم يظاهروا عليكم, باللغة نيانجا

﴿إلا الذين عاهدتم من المشركين ثم لم ينقصوكم شيئا ولم يظاهروا عليكم﴾ [التوبَة: 4]

Khaled Ibrahim Betala
“Kupatula ena amene mudapangana nawo mapangano mwa Amushirikina, (omwe adasunga mapangano awo), kenako sadapungule chilichonse ndipo sadathandize aliyense pa inu, akwaniritseni mapangano awo mpaka m’nyengo yawo. Ndithu Allah akukonda amene akumuopa (ndi kusunga mapangano)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek