×

Motero usalole kuti chuma chawo kapena ana awo kuti akudabwitse. Cholinga cha 9:55 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:55) ayat 55 in Chichewa

9:55 Surah At-Taubah ayat 55 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 55 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿فَلَا تُعۡجِبۡكَ أَمۡوَٰلُهُمۡ وَلَآ أَوۡلَٰدُهُمۡۚ إِنَّمَا يُرِيدُ ٱللَّهُ لِيُعَذِّبَهُم بِهَا فِي ٱلۡحَيَوٰةِ ٱلدُّنۡيَا وَتَزۡهَقَ أَنفُسُهُمۡ وَهُمۡ كَٰفِرُونَ ﴾
[التوبَة: 55]

Motero usalole kuti chuma chawo kapena ana awo kuti akudabwitse. Cholinga cha Mulungu ndikufuna kuwalanga ndi izi m’moyo uno ndipo kuti mizimu yawo idzachoke pamene iwo ali osakhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فلا تعجبك أموالهم ولا أولادهم إنما يريد الله ليعذبهم بها في الحياة, باللغة نيانجا

﴿فلا تعجبك أموالهم ولا أولادهم إنما يريد الله ليعذبهم بها في الحياة﴾ [التوبَة: 55]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo chisakudolole chuma chawo kapena ana awo. Ndithu Allah akufuna kuwalanga nazo pa moyo wa pa dziko lapansi, ndi kuti mitima yawo ichoke ali osakhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek