×

Palibe chimene chaletsa kuti zopereka zawo zilandiridwe kupatula kuti iwo sanakhulupilire mwa 9:54 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:54) ayat 54 in Chichewa

9:54 Surah At-Taubah ayat 54 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 54 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿وَمَا مَنَعَهُمۡ أَن تُقۡبَلَ مِنۡهُمۡ نَفَقَٰتُهُمۡ إِلَّآ أَنَّهُمۡ كَفَرُواْ بِٱللَّهِ وَبِرَسُولِهِۦ وَلَا يَأۡتُونَ ٱلصَّلَوٰةَ إِلَّا وَهُمۡ كُسَالَىٰ وَلَا يُنفِقُونَ إِلَّا وَهُمۡ كَٰرِهُونَ ﴾
[التوبَة: 54]

Palibe chimene chaletsa kuti zopereka zawo zilandiridwe kupatula kuti iwo sanakhulupilire mwa Mulungu ndi Mtumwi wake ndipo iwo samabwera ku mapemphero kupatula mwaulesi ndipo samapereka zopereka zawo kupatula modandaula

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما منعهم أن تقبل منهم نفقاتهم إلا أنهم كفروا بالله وبرسوله ولا, باللغة نيانجا

﴿وما منعهم أن تقبل منهم نفقاتهم إلا أنهم كفروا بالله وبرسوله ولا﴾ [التوبَة: 54]

Khaled Ibrahim Betala
“Palibe chomwe chidaletsa kulandiridwa kwa zopereka zawo koma chifukwa chakuti iwo sadakhulupirire Allah ndi Mtumiki Wake; ndiponso sapita kopemphera koma mwaulesi; ndipo sapereka chopereka koma monyinyirika
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek