×

Motero Iye adawalanga pokhazikitsa chinyengo m’mitima mwawo mpaka pa tsiku limene iwo 9:77 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:77) ayat 77 in Chichewa

9:77 Surah At-Taubah ayat 77 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 77 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿فَأَعۡقَبَهُمۡ نِفَاقٗا فِي قُلُوبِهِمۡ إِلَىٰ يَوۡمِ يَلۡقَوۡنَهُۥ بِمَآ أَخۡلَفُواْ ٱللَّهَ مَا وَعَدُوهُ وَبِمَا كَانُواْ يَكۡذِبُونَ ﴾
[التوبَة: 77]

Motero Iye adawalanga pokhazikitsa chinyengo m’mitima mwawo mpaka pa tsiku limene iwo adzakumana Naye, chifukwa chakuphwanya kwawo zimene analonjeza kwa Iye ndi chifukwa chakulankhula kwawo kwabodza

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فأعقبهم نفاقا في قلوبهم إلى يوم يلقونه بما أخلفوا الله ما وعدوه, باللغة نيانجا

﴿فأعقبهم نفاقا في قلوبهم إلى يوم يلقونه بما أخلفوا الله ما وعدوه﴾ [التوبَة: 77]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho, chotsatira chake adawaika chinyengo m’mitima mwawo kufikira tsiku lokumana naye (Allah), chifukwa cha kuphwanya kwawo zomwe adamulonjeza Allah. Ndiponso chifukwa cha zabodza zomwe ankanena
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek