Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 84 - التوبَة - Page - Juz 10
﴿وَلَا تُصَلِّ عَلَىٰٓ أَحَدٖ مِّنۡهُم مَّاتَ أَبَدٗا وَلَا تَقُمۡ عَلَىٰ قَبۡرِهِۦٓۖ إِنَّهُمۡ كَفَرُواْ بِٱللَّهِ وَرَسُولِهِۦ وَمَاتُواْ وَهُمۡ فَٰسِقُونَ ﴾
[التوبَة: 84]
﴿ولا تصل على أحد منهم مات أبدا ولا تقم على قبره إنهم﴾ [التوبَة: 84]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo usamupemphelere konse aliyense wa iwo yemwe wamwalira, ndipo usaimilire pamanda ake (kumpemphelera); ndithu iwo amukana Allah ndi Mtumiki Wake, ndipo amwalira uku ali opandukira chilamulo (cha Allah) |