×

Maarabu amene amakhala m’chipululu ndiwo oipa kwambiri posakhulupirira ndi m’chinyengo, ndipo ndi 9:97 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:97) ayat 97 in Chichewa

9:97 Surah At-Taubah ayat 97 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 97 - التوبَة - Page - Juz 11

﴿ٱلۡأَعۡرَابُ أَشَدُّ كُفۡرٗا وَنِفَاقٗا وَأَجۡدَرُ أَلَّا يَعۡلَمُواْ حُدُودَ مَآ أَنزَلَ ٱللَّهُ عَلَىٰ رَسُولِهِۦۗ وَٱللَّهُ عَلِيمٌ حَكِيمٞ ﴾
[التوبَة: 97]

Maarabu amene amakhala m’chipululu ndiwo oipa kwambiri posakhulupirira ndi m’chinyengo, ndipo ndi oyenera kusadziwa malire amene Mulungu wavumbulutsa kwa Mtumwiwake. Ndipo Mulunguamadziwazinthuzonse ndipo ndi Wanzeru

❮ Previous Next ❯

ترجمة: الأعراب أشد كفرا ونفاقا وأجدر ألا يعلموا حدود ما أنـزل الله على, باللغة نيانجا

﴿الأعراب أشد كفرا ونفاقا وأجدر ألا يعلموا حدود ما أنـزل الله على﴾ [التوبَة: 97]

Khaled Ibrahim Betala
“Arabu a kumizi ngoyipitsitsa pa kusakhulupirira ndi uchiphamaso ndiponso ngoyenera kusazindikira malire a zomwe Allah wavumbulutsa kwa Mtumiki Wake. Komatu Allah Ngodziwa kwambiri, Ngwanzeru zakuya
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek