×

Ndithudi mosakaika Mulungu ndiye Mwini wa chilichonse chimene chili mlengalenga ndi padziko 10:55 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yunus ⮕ (10:55) ayat 55 in Chichewa

10:55 Surah Yunus ayat 55 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yunus ayat 55 - يُونس - Page - Juz 11

﴿أَلَآ إِنَّ لِلَّهِ مَا فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِۗ أَلَآ إِنَّ وَعۡدَ ٱللَّهِ حَقّٞ وَلَٰكِنَّ أَكۡثَرَهُمۡ لَا يَعۡلَمُونَ ﴾
[يُونس: 55]

Ndithudi mosakaika Mulungu ndiye Mwini wa chilichonse chimene chili mlengalenga ndi padziko lapansi. Ndithudi mosakaika lonjezo la Mulungu ndi loona. Koma ambiri a iwo sadziwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ألا إن لله ما في السموات والأرض ألا إن وعد الله حق, باللغة نيانجا

﴿ألا إن لله ما في السموات والأرض ألا إن وعد الله حق﴾ [يُونس: 55]

Khaled Ibrahim Betala
“Tamverani! Ndithu zonse za kumwamba ndi pansi nza Allah. Tamverani! Ndithu lonjezo la Allah ndi loona, koma ambiri a iwo sadziwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek