Quran with Chichewa translation - Surah Yunus ayat 57 - يُونس - Page - Juz 11
﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلنَّاسُ قَدۡ جَآءَتۡكُم مَّوۡعِظَةٞ مِّن رَّبِّكُمۡ وَشِفَآءٞ لِّمَا فِي ٱلصُّدُورِ وَهُدٗى وَرَحۡمَةٞ لِّلۡمُؤۡمِنِينَ ﴾
[يُونس: 57]
﴿ياأيها الناس قد جاءتكم موعظة من ربكم وشفاء لما في الصدور وهدى﴾ [يُونس: 57]
Khaled Ibrahim Betala “E inu anthu! Ndithu ulaliki wakudzerani kuchokera kwa Mbuye wanu ndi machiritso a matenda omwe ali m’mitima mwanu, ndiponso nchiongoko ndi chifundo kwa okhulupirira |