Quran with Chichewa translation - Surah Yunus ayat 7 - يُونس - Page - Juz 11
﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ لَا يَرۡجُونَ لِقَآءَنَا وَرَضُواْ بِٱلۡحَيَوٰةِ ٱلدُّنۡيَا وَٱطۡمَأَنُّواْ بِهَا وَٱلَّذِينَ هُمۡ عَنۡ ءَايَٰتِنَا غَٰفِلُونَ ﴾
[يُونس: 7]
﴿إن الذين لا يرجون لقاءنا ورضوا بالحياة الدنيا واطمأنوا بها والذين هم﴾ [يُونس: 7]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu amene sayembekeza kukumana Nafe, nakondetsetsa umoyo wapadziko lapansi ndi kukhazikika (mtima) ndi za mmenemo, ndi omwe akunyozera Ayah Zathu |