×

Ndithudi mukasinthidwe ka usiku ndi usana ndi zimene Mulungu walenga kumwamba ndi 10:6 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yunus ⮕ (10:6) ayat 6 in Chichewa

10:6 Surah Yunus ayat 6 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yunus ayat 6 - يُونس - Page - Juz 11

﴿إِنَّ فِي ٱخۡتِلَٰفِ ٱلَّيۡلِ وَٱلنَّهَارِ وَمَا خَلَقَ ٱللَّهُ فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِ لَأٓيَٰتٖ لِّقَوۡمٖ يَتَّقُونَ ﴾
[يُونس: 6]

Ndithudi mukasinthidwe ka usiku ndi usana ndi zimene Mulungu walenga kumwamba ndi dziko lapansi, muli zizindikiro kwa anthu okana uchimo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن في اختلاف الليل والنهار وما خلق الله في السموات والأرض لآيات, باللغة نيانجا

﴿إن في اختلاف الليل والنهار وما خلق الله في السموات والأرض لآيات﴾ [يُونس: 6]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu m’kusinthanasinthana kwa usiku ndi usana, ndi zomwe Allah walenga kumwamba ndi pansi, ndithudi, ndi zisonyezo kwa anthu oopa (Allah)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek