Quran with Chichewa translation - Surah Al-Humazah ayat 1 - الهُمَزة - Page - Juz 30
﴿وَيۡلٞ لِّكُلِّ هُمَزَةٖ لُّمَزَةٍ ﴾
[الهُمَزة: 1]
﴿ويل لكل همزة لمزة﴾ [الهُمَزة: 1]
Khaled Ibrahim Betala “Kuonongeka koopsa kudzampeza aliyense wojeda ndi wonyoza anthu polozera (ndi maso kapena kuyankhula ndi lirime) |