Quran with Chichewa translation - Surah Hud ayat 120 - هُود - Page - Juz 12
﴿وَكُلّٗا نَّقُصُّ عَلَيۡكَ مِنۡ أَنۢبَآءِ ٱلرُّسُلِ مَا نُثَبِّتُ بِهِۦ فُؤَادَكَۚ وَجَآءَكَ فِي هَٰذِهِ ٱلۡحَقُّ وَمَوۡعِظَةٞ وَذِكۡرَىٰ لِلۡمُؤۡمِنِينَ ﴾
[هُود: 120]
﴿وكلا نقص عليك من أنباء الرسل ما نثبت به فؤادك وجاءك في﴾ [هُود: 120]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo tikukusimbira zonse mwa nkhani za atumiki zomwe tikukulimbikitsa nazo mtima. Ndipo m’zimenezi choonadi chakufika ndi ulaliki ndiponso chikumbutso kwa okhulupirira |