×

Akapanda kukuyankha, dziwa kuti chivumbulutso chatumizidwa ndi nzeru ya Mulungu. Ndipo kuti 11:14 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Hud ⮕ (11:14) ayat 14 in Chichewa

11:14 Surah Hud ayat 14 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Hud ayat 14 - هُود - Page - Juz 12

﴿فَإِلَّمۡ يَسۡتَجِيبُواْ لَكُمۡ فَٱعۡلَمُوٓاْ أَنَّمَآ أُنزِلَ بِعِلۡمِ ٱللَّهِ وَأَن لَّآ إِلَٰهَ إِلَّا هُوَۖ فَهَلۡ أَنتُم مُّسۡلِمُونَ ﴾
[هُود: 14]

Akapanda kukuyankha, dziwa kuti chivumbulutso chatumizidwa ndi nzeru ya Mulungu. Ndipo kuti kulibe wina woti apembedzedwe kupatula Iye yekha. Kodi tsopano mudzakhala ogonjera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فإلم يستجيبوا لكم فاعلموا أنما أنـزل بعلم الله وأن لا إله إلا, باللغة نيانجا

﴿فإلم يستجيبوا لكم فاعلموا أنما أنـزل بعلم الله وأن لا إله إلا﴾ [هُود: 14]

Khaled Ibrahim Betala
““Ngati sakuyankhani, choncho, dziwani kuti yavumbulutsidwa (Qur’aniyo) m’kudziwa kwa Allah, ndikuti kulibe mulungu wina koma Iye. Nanga kodi inu simugonjera (Iye)?”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek