Quran with Chichewa translation - Surah Hud ayat 36 - هُود - Page - Juz 12
﴿وَأُوحِيَ إِلَىٰ نُوحٍ أَنَّهُۥ لَن يُؤۡمِنَ مِن قَوۡمِكَ إِلَّا مَن قَدۡ ءَامَنَ فَلَا تَبۡتَئِسۡ بِمَا كَانُواْ يَفۡعَلُونَ ﴾
[هُود: 36]
﴿وأوحي إلى نوح أنه لن يؤمن من قومك إلا من قد آمن﴾ [هُود: 36]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo tidamuululira Nuh kuti: “(Tsopano) sakhulupirira aliyense mwa anthu ako kupatula okhawo akhulupirira kale. Choncho, usadandaule pa zimene adali kuchita.” |