×

“Ndipo inu mudzadziwa posachedwa yemwe chilango chochititsa manyazi chidzamfikira, ndiponso iwo amene 11:39 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Hud ⮕ (11:39) ayat 39 in Chichewa

11:39 Surah Hud ayat 39 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Hud ayat 39 - هُود - Page - Juz 12

﴿فَسَوۡفَ تَعۡلَمُونَ مَن يَأۡتِيهِ عَذَابٞ يُخۡزِيهِ وَيَحِلُّ عَلَيۡهِ عَذَابٞ مُّقِيمٌ ﴾
[هُود: 39]

“Ndipo inu mudzadziwa posachedwa yemwe chilango chochititsa manyazi chidzamfikira, ndiponso iwo amene adzalandira chilango chosatha.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فسوف تعلمون من يأتيه عذاب يخزيه ويحل عليه عذاب مقيم, باللغة نيانجا

﴿فسوف تعلمون من يأتيه عذاب يخزيه ويحل عليه عذاب مقيم﴾ [هُود: 39]

Khaled Ibrahim Betala
““Posachedwa mudziwa kuti ndani chimdzere chilango chomuyalutsa ndi kumtsikira chilango chopitilira.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek