Quran with Chichewa translation - Surah Hud ayat 90 - هُود - Page - Juz 12
﴿وَٱسۡتَغۡفِرُواْ رَبَّكُمۡ ثُمَّ تُوبُوٓاْ إِلَيۡهِۚ إِنَّ رَبِّي رَحِيمٞ وَدُودٞ ﴾
[هُود: 90]
﴿واستغفروا ربكم ثم توبوا إليه إن ربي رحيم ودود﴾ [هُود: 90]
Khaled Ibrahim Betala ““Ndipo mpempheni chikhululuko Mbuye wanu ndipo lapani kwa Iye (posiya machimo ndikuchita zabwino). Ndithu Mbuye wanga Ngwachisoni Ngwachikondi chochuluka (kwa anthu Ake).” |