Quran with Chichewa translation - Surah Hud ayat 99 - هُود - Page - Juz 12
﴿وَأُتۡبِعُواْ فِي هَٰذِهِۦ لَعۡنَةٗ وَيَوۡمَ ٱلۡقِيَٰمَةِۚ بِئۡسَ ٱلرِّفۡدُ ٱلۡمَرۡفُودُ ﴾
[هُود: 99]
﴿وأتبعوا في هذه لعنة ويوم القيامة بئس الرفد المرفود﴾ [هُود: 99]
Khaled Ibrahim Betala “Iwo adatsatizidwa ndi tembelero pano pa dziko lapansi ndipo pa tsiku la Qiyâma (adzatsatizidwanso). Taonani kuipa mphoto (yawo) yopatsidwa |