×

Ndipo pamene iwo adapita naye, iwo adagwirizana zomuponya m’chitsime chamdima ndipo Ife 12:15 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:15) ayat 15 in Chichewa

12:15 Surah Yusuf ayat 15 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 15 - يُوسُف - Page - Juz 12

﴿فَلَمَّا ذَهَبُواْ بِهِۦ وَأَجۡمَعُوٓاْ أَن يَجۡعَلُوهُ فِي غَيَٰبَتِ ٱلۡجُبِّۚ وَأَوۡحَيۡنَآ إِلَيۡهِ لَتُنَبِّئَنَّهُم بِأَمۡرِهِمۡ هَٰذَا وَهُمۡ لَا يَشۡعُرُونَ ﴾
[يُوسُف: 15]

Ndipo pamene iwo adapita naye, iwo adagwirizana zomuponya m’chitsime chamdima ndipo Ife tidamuuza iye kuti, “Iwe udzawauza zonsezi nthawi ina pamene iwo sakudziwa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فلما ذهبوا به وأجمعوا أن يجعلوه في غيابت الجب وأوحينا إليه لتنبئنهم, باللغة نيانجا

﴿فلما ذهبوا به وأجمعوا أن يجعلوه في غيابت الجب وأوحينا إليه لتنبئنهم﴾ [يُوسُف: 15]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo pamene adanka naye ndi kugwirizana pakati pawo kuti amuike mchitsime chakuya, (adamuikadi). Ndipo tidamzindikiritsa iye (Yûsuf): “Ndithu udzawauza chinthu chawochi (chimene akuchitirachi) pomwe iwo sakudziwa.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek