Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 53 - يُوسُف - Page - Juz 13
﴿۞ وَمَآ أُبَرِّئُ نَفۡسِيٓۚ إِنَّ ٱلنَّفۡسَ لَأَمَّارَةُۢ بِٱلسُّوٓءِ إِلَّا مَا رَحِمَ رَبِّيٓۚ إِنَّ رَبِّي غَفُورٞ رَّحِيمٞ ﴾
[يُوسُف: 53]
﴿وما أبرئ نفسي إن النفس لأمارة بالسوء إلا ما رحم ربي إن﴾ [يُوسُف: 53]
Khaled Ibrahim Betala “۞ “Ndipo ine sindikuyeretsa mtima wanga. Ndithu mtima uliwonse umalamulira kwambiri ku zoipa kupatula umene Mbuye wanga wauchitira chifundo. Ndithudi, Mbuye wanga Ngokhululuka, Ngwachisoni chosatha.” |