×

Ndipo iye adati, “E inu ana anga! Musakalowere khomo limodzi koma kaloweni 12:67 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:67) ayat 67 in Chichewa

12:67 Surah Yusuf ayat 67 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 67 - يُوسُف - Page - Juz 13

﴿وَقَالَ يَٰبَنِيَّ لَا تَدۡخُلُواْ مِنۢ بَابٖ وَٰحِدٖ وَٱدۡخُلُواْ مِنۡ أَبۡوَٰبٖ مُّتَفَرِّقَةٖۖ وَمَآ أُغۡنِي عَنكُم مِّنَ ٱللَّهِ مِن شَيۡءٍۖ إِنِ ٱلۡحُكۡمُ إِلَّا لِلَّهِۖ عَلَيۡهِ تَوَكَّلۡتُۖ وَعَلَيۡهِ فَلۡيَتَوَكَّلِ ٱلۡمُتَوَكِّلُونَ ﴾
[يُوسُف: 67]

Ndipo iye adati, “E inu ana anga! Musakalowere khomo limodzi koma kaloweni m’makomo osiyanasiyana ndipo ine sindingakuthandizeni chilichonse polimbana ndi Mulungu. Zoonadi chiweruzo ndi cha Mulungu yekha. Mwa Iye yekha ine ndimaika chikhulupiriro changa ndipo onse amene amakhulupirira aike chikhulupiriro chawo mwa Iye.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقال يابني لا تدخلوا من باب واحد وادخلوا من أبواب متفرقة وما, باللغة نيانجا

﴿وقال يابني لا تدخلوا من باب واحد وادخلوا من أبواب متفرقة وما﴾ [يُوسُف: 67]

Khaled Ibrahim Betala
“Adatinso: “E inu ana anga! Musakalowe (mu Iguputo) pachipata chimodzi koma kaloweni pa zipata zosiyanasiyana. Ndipo sindingakuthandizeni chilichonse kwa Allah. Lamulo ndi la Allah basi; kwa Iye ndiko ndatsamira; ndipo otsamira atsamire kwa Iye.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek