×

Iye adati, “Ine sindidzamutumiza iye pamodzi ndi inu pokhapokha ngati mutandipatsalonjezoM’dzinalaMulungu,kutimudzabwera naye 12:66 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:66) ayat 66 in Chichewa

12:66 Surah Yusuf ayat 66 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 66 - يُوسُف - Page - Juz 13

﴿قَالَ لَنۡ أُرۡسِلَهُۥ مَعَكُمۡ حَتَّىٰ تُؤۡتُونِ مَوۡثِقٗا مِّنَ ٱللَّهِ لَتَأۡتُنَّنِي بِهِۦٓ إِلَّآ أَن يُحَاطَ بِكُمۡۖ فَلَمَّآ ءَاتَوۡهُ مَوۡثِقَهُمۡ قَالَ ٱللَّهُ عَلَىٰ مَا نَقُولُ وَكِيلٞ ﴾
[يُوسُف: 66]

Iye adati, “Ine sindidzamutumiza iye pamodzi ndi inu pokhapokha ngati mutandipatsalonjezoM’dzinalaMulungu,kutimudzabwera naye kwa ine kupatula ngati mutagonjetsedwa.” Ndipo pamene iwo adapereka lonjezo lawo, iye adanena kuti, “Pa zonse zimene tikunena, Mulungu akhale mboni.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال لن أرسله معكم حتى تؤتون موثقا من الله لتأتنني به إلا, باللغة نيانجا

﴿قال لن أرسله معكم حتى تؤتون موثقا من الله لتأتنني به إلا﴾ [يُوسُف: 66]

Khaled Ibrahim Betala
“(Ya’qub) adati: “Sindingamtumize pamodzi ndi inu pokhapokha mundipatse lonjezo m’dzina la Allah kuti ndithudi mudzambweza kwa ine pokhapokha nonsenu mutazingidwa (ndi zoopsa).” Ndipo pamene adapereka lonjezo lawo, (iye) adati: “Allah ndiye Muyang’aniri (mboni) pa zimene tikunenazi.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek