×

Iwo adati, “Ngati iye waba, ndiye kuti panali m’bale wake wina amene 12:77 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:77) ayat 77 in Chichewa

12:77 Surah Yusuf ayat 77 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 77 - يُوسُف - Page - Juz 13

﴿۞ قَالُوٓاْ إِن يَسۡرِقۡ فَقَدۡ سَرَقَ أَخٞ لَّهُۥ مِن قَبۡلُۚ فَأَسَرَّهَا يُوسُفُ فِي نَفۡسِهِۦ وَلَمۡ يُبۡدِهَا لَهُمۡۚ قَالَ أَنتُمۡ شَرّٞ مَّكَانٗاۖ وَٱللَّهُ أَعۡلَمُ بِمَا تَصِفُونَ ﴾
[يُوسُف: 77]

Iwo adati, “Ngati iye waba, ndiye kuti panali m’bale wake wina amene adabanso kale.” Koma Yosefe adasunga chinsinsi ndipo sadawauze iwo ayi. Iye adaganiza kuti “Inu muli pa mlandu. Mulungu ali kudziwa bwino zonse zimene mukunena.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قالوا إن يسرق فقد سرق أخ له من قبل فأسرها يوسف في, باللغة نيانجا

﴿قالوا إن يسرق فقد سرق أخ له من قبل فأسرها يوسف في﴾ [يُوسُف: 77]

Khaled Ibrahim Betala
“(Iwo) adati: “Ngati waba, m’bale wakenso adabapo kale.” (Uku kudali kumunamizira Yûsuf bodza pomwe iwo sankadziwa kuti yemwe akuyankhula nayeyo ndiye Yûsuf). Koma Yûsuf adabisa (mawu awa) mu mtima mwake, (chifukwa chowamvera chisoni) ndipo sadawaululire. Adati: “Inu muli ndi chikhalidwe choipa ndipo Allah akudziwa zomwe mukunena!”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek