×

“oh ana anga!, Pitani mukafufuze za Yosefe pamodzi ndi m’bale wake, ndipo 12:87 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:87) ayat 87 in Chichewa

12:87 Surah Yusuf ayat 87 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 87 - يُوسُف - Page - Juz 13

﴿يَٰبَنِيَّ ٱذۡهَبُواْ فَتَحَسَّسُواْ مِن يُوسُفَ وَأَخِيهِ وَلَا تَاْيۡـَٔسُواْ مِن رَّوۡحِ ٱللَّهِۖ إِنَّهُۥ لَا يَاْيۡـَٔسُ مِن رَّوۡحِ ٱللَّهِ إِلَّا ٱلۡقَوۡمُ ٱلۡكَٰفِرُونَ ﴾
[يُوسُف: 87]

“oh ana anga!, Pitani mukafufuze za Yosefe pamodzi ndi m’bale wake, ndipo musataye mtima ndi chisomo cha Mulungu. Ndithudi palibe amene amataya mtima ndi chisomo cha Mulungu kupatula anthu osakhulupirira.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: يابني اذهبوا فتحسسوا من يوسف وأخيه ولا تيأسوا من روح الله إنه, باللغة نيانجا

﴿يابني اذهبوا فتحسسوا من يوسف وأخيه ولا تيأسوا من روح الله إنه﴾ [يُوسُف: 87]

Khaled Ibrahim Betala
““E ana anga! Pitani mukafufuzefufuze za Yûsuf ndi m’bale wake, ndipo musataye mtima pa chifundo cha Allah. Ndithu palibe amene amataya mtima za chifundo cha Allah koma anthu osakhulupirira.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek