×

Iwo adati, “Kodi iwe ndiwedi Yosefe?” Iye adati, “Ine ndine Yosefe ndipo 12:90 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:90) ayat 90 in Chichewa

12:90 Surah Yusuf ayat 90 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 90 - يُوسُف - Page - Juz 13

﴿قَالُوٓاْ أَءِنَّكَ لَأَنتَ يُوسُفُۖ قَالَ أَنَا۠ يُوسُفُ وَهَٰذَآ أَخِيۖ قَدۡ مَنَّ ٱللَّهُ عَلَيۡنَآۖ إِنَّهُۥ مَن يَتَّقِ وَيَصۡبِرۡ فَإِنَّ ٱللَّهَ لَا يُضِيعُ أَجۡرَ ٱلۡمُحۡسِنِينَ ﴾
[يُوسُف: 90]

Iwo adati, “Kodi iwe ndiwedi Yosefe?” Iye adati, “Ine ndine Yosefe ndipo uyu ndi m’bale wanga. Mulungu, ndithudi, watikomera mtima ife. Ndithudi iye amene amaopa Mulungu ndi kupirira molimba ndithudi Mulungu sasokoneza malipiro a anthu ochita zabwino.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قالوا أئنك لأنت يوسف قال أنا يوسف وهذا أخي قد من الله, باللغة نيانجا

﴿قالوا أئنك لأنت يوسف قال أنا يوسف وهذا أخي قد من الله﴾ [يُوسُف: 90]

Khaled Ibrahim Betala
“(Iwo) adati: “Kodi iwe ndiwe Yûsuf?” Adati: “Ine ndine Yûsuf, ndipo uyu ndi m’bale wanga; Allah watichitira zabwino. Ndithu amene aopa Allah ndikumapirira, (Allah amulipira). Ndithu Allah sasokoneza malipiro a ochita zabwino.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek