×

Kotero Ife talitumiza pansi kukhala chiweruzo champhamvu m’chiyankhulo cha Chiarabu. Ngati iwe 13:37 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ar-Ra‘d ⮕ (13:37) ayat 37 in Chichewa

13:37 Surah Ar-Ra‘d ayat 37 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Ra‘d ayat 37 - الرَّعد - Page - Juz 13

﴿وَكَذَٰلِكَ أَنزَلۡنَٰهُ حُكۡمًا عَرَبِيّٗاۚ وَلَئِنِ ٱتَّبَعۡتَ أَهۡوَآءَهُم بَعۡدَ مَا جَآءَكَ مِنَ ٱلۡعِلۡمِ مَا لَكَ مِنَ ٱللَّهِ مِن وَلِيّٖ وَلَا وَاقٖ ﴾
[الرَّعد: 37]

Kotero Ife talitumiza pansi kukhala chiweruzo champhamvu m’chiyankhulo cha Chiarabu. Ngati iwe utsatira zofuna zawo pamene utapatsidwa nzeru, palibe amene adzakupulumutsa kapena kukuteteza kwa Mulungu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وكذلك أنـزلناه حكما عربيا ولئن اتبعت أهواءهم بعد ما جاءك من العلم, باللغة نيانجا

﴿وكذلك أنـزلناه حكما عربيا ولئن اتبعت أهواءهم بعد ما جاءك من العلم﴾ [الرَّعد: 37]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo momwemo taivumbulutsa (iyi Qur’an) m’Chiarabu kuti ikhale chilamulo (cha Allah). Ngati utsata zofuna zawo pambuyo pokufika kuzindikiraku, sudzakhala ndi bwenzi ngakhale mtetezi kwa Allah
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek