×

Kodi iwe siuona kuti Mulungu adalenga kumwamba ndi dziko lapansi mwachoonadi? Atafuna 14:19 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ibrahim ⮕ (14:19) ayat 19 in Chichewa

14:19 Surah Ibrahim ayat 19 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 19 - إبراهِيم - Page - Juz 13

﴿أَلَمۡ تَرَ أَنَّ ٱللَّهَ خَلَقَ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضَ بِٱلۡحَقِّۚ إِن يَشَأۡ يُذۡهِبۡكُمۡ وَيَأۡتِ بِخَلۡقٖ جَدِيدٖ ﴾
[إبراهِيم: 19]

Kodi iwe siuona kuti Mulungu adalenga kumwamba ndi dziko lapansi mwachoonadi? Atafuna Iye akhoza kukuchotsani ndi kubweretsa zolengedwa zatsopano

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ألم تر أن الله خلق السموات والأرض بالحق إن يشأ يذهبكم ويأت, باللغة نيانجا

﴿ألم تر أن الله خلق السموات والأرض بالحق إن يشأ يذهبكم ويأت﴾ [إبراهِيم: 19]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi siuona kuti Allah adalenga thambo ndi nthaka mwachoonadi? Ndipo atafuna angakuchotseni (nthawi imodzi) ndikubweretsa zolengedwa zina zatsopano
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek