×

Fanizo la iwo amene sakhulupirira mwa Ambuye wawo ndi lakuti ntchito zawo 14:18 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ibrahim ⮕ (14:18) ayat 18 in Chichewa

14:18 Surah Ibrahim ayat 18 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 18 - إبراهِيم - Page - Juz 13

﴿مَّثَلُ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ بِرَبِّهِمۡۖ أَعۡمَٰلُهُمۡ كَرَمَادٍ ٱشۡتَدَّتۡ بِهِ ٱلرِّيحُ فِي يَوۡمٍ عَاصِفٖۖ لَّا يَقۡدِرُونَ مِمَّا كَسَبُواْ عَلَىٰ شَيۡءٖۚ ذَٰلِكَ هُوَ ٱلضَّلَٰلُ ٱلۡبَعِيدُ ﴾
[إبراهِيم: 18]

Fanizo la iwo amene sakhulupirira mwa Ambuye wawo ndi lakuti ntchito zawo zili ngati phulusa limene liulutsidwa ndi mphepo pa tsiku la mphepo ya mkuntho. Iwo sadzapeza china chilichonse kuchokera ku zinthu zimene ankachita. Ndipo kumeneku ndiko kusochera kwenikweni

❮ Previous Next ❯

ترجمة: مثل الذين كفروا بربهم أعمالهم كرماد اشتدت به الريح في يوم عاصف, باللغة نيانجا

﴿مثل الذين كفروا بربهم أعمالهم كرماد اشتدت به الريح في يوم عاصف﴾ [إبراهِيم: 18]

Khaled Ibrahim Betala
“Fanizo la amene sadakhulupirire Mbuye wawo, zochita zawo (zabwino zomwe sadzalipidwa nazo chabwino chilichonse chifukwa chakuti sadazichite pofuna kukondweretsa Allah) zili ngati phulusa lomwe likuulutsidwa ndi mphepo ya mkuntho; ndipo sadzatha kupindula chilichonse pa zimene adachita, uko ndikutaika konka nako kutali (ndi choonadi)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek