×

Iwo akhazikitsa milungu yabodza kuti ikhale yofanana ndi Mulungu ndi cholinga chosokoneza 14:30 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ibrahim ⮕ (14:30) ayat 30 in Chichewa

14:30 Surah Ibrahim ayat 30 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 30 - إبراهِيم - Page - Juz 13

﴿وَجَعَلُواْ لِلَّهِ أَندَادٗا لِّيُضِلُّواْ عَن سَبِيلِهِۦۗ قُلۡ تَمَتَّعُواْ فَإِنَّ مَصِيرَكُمۡ إِلَى ٱلنَّارِ ﴾
[إبراهِيم: 30]

Iwo akhazikitsa milungu yabodza kuti ikhale yofanana ndi Mulungu ndi cholinga chosokoneza anthu ku njira yake. Nena, “Basangalalani! Koma, ndithudi, kokafikira kwanu ndi ku Moto.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وجعلوا لله أندادا ليضلوا عن سبيله قل تمتعوا فإن مصيركم إلى النار, باللغة نيانجا

﴿وجعلوا لله أندادا ليضلوا عن سبيله قل تمتعوا فإن مصيركم إلى النار﴾ [إبراهِيم: 30]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ampangira Allah anzake kuti asokeretse (anthu) kunjira Yake! Nena: “Sangalalani pang’ono chabe! Ndithu kobwerera kwanu nkuMoto!”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek