×

Auze akapolo anga, amene ali okhulupirira kuti apitirize mapemphero ndi kupereka zothandiza 14:31 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ibrahim ⮕ (14:31) ayat 31 in Chichewa

14:31 Surah Ibrahim ayat 31 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 31 - إبراهِيم - Page - Juz 13

﴿قُل لِّعِبَادِيَ ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ يُقِيمُواْ ٱلصَّلَوٰةَ وَيُنفِقُواْ مِمَّا رَزَقۡنَٰهُمۡ سِرّٗا وَعَلَانِيَةٗ مِّن قَبۡلِ أَن يَأۡتِيَ يَوۡمٞ لَّا بَيۡعٞ فِيهِ وَلَا خِلَٰلٌ ﴾
[إبراهِيم: 31]

Auze akapolo anga, amene ali okhulupirira kuti apitirize mapemphero ndi kupereka zothandiza osauka kuchokera ku zimene tawapatsa mseri ndi pooneka, lisanafike tsiku limene sikudzakhala kukambirana kapena kuchita ubwenzi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل لعبادي الذين آمنوا يقيموا الصلاة وينفقوا مما رزقناهم سرا وعلانية من, باللغة نيانجا

﴿قل لعبادي الذين آمنوا يقيموا الصلاة وينفقوا مما رزقناهم سرا وعلانية من﴾ [إبراهِيم: 31]

Khaled Ibrahim Betala
“Auze akapolo Anga amene akhulupirira kuti apemphere Swala ndikupereka zina mwa zomwe tawapatsa, mobisa ndi moonekera lisanawafike tsiku lopanda (chithandizo cha) kudziombola ndi (chithandizo cha) ubwenzi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek