Quran with Chichewa translation - Surah Al-hijr ayat 56 - الحِجر - Page - Juz 14
﴿قَالَ وَمَن يَقۡنَطُ مِن رَّحۡمَةِ رَبِّهِۦٓ إِلَّا ٱلضَّآلُّونَ ﴾
[الحِجر: 56]
﴿قال ومن يقنط من رحمة ربه إلا الضالون﴾ [الحِجر: 56]
Khaled Ibrahim Betala “Iye adati: “(Ine sinditaya mtima ndi chifundo cha Allah. Ndipo) palibe angataye mtima ndi chifundo cha Allah, koma wosokera basi (yemwe sazindikira ukulu wa Allah).” |