Quran with Chichewa translation - Surah Al-hijr ayat 67 - الحِجر - Page - Juz 14
﴿وَجَآءَ أَهۡلُ ٱلۡمَدِينَةِ يَسۡتَبۡشِرُونَ ﴾
[الحِجر: 67]
﴿وجاء أهل المدينة يستبشرون﴾ [الحِجر: 67]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo adadza (kwa Luti) anthu a m’mudziwo akusangalala (poona kuti kwadza alendo okongola kuti achite nawo zadama) |