Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 103 - النَّحل - Page - Juz 14
﴿وَلَقَدۡ نَعۡلَمُ أَنَّهُمۡ يَقُولُونَ إِنَّمَا يُعَلِّمُهُۥ بَشَرٞۗ لِّسَانُ ٱلَّذِي يُلۡحِدُونَ إِلَيۡهِ أَعۡجَمِيّٞ وَهَٰذَا لِسَانٌ عَرَبِيّٞ مُّبِينٌ ﴾
[النَّحل: 103]
﴿ولقد نعلم أنهم يقولون إنما يعلمه بشر لسان الذي يلحدون إليه أعجمي﴾ [النَّحل: 103]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu tikudziwa kuti iwo akunena: “Pali munthu amene akumphunzitsa.” (Koma) chiyankhulo cha amene akumganizirayo nchachilendo, ndipo ichi (chiyankhulo cha Qur’an) ndi chiyankhulo cha Chiarabu chomveka |