×

Motero idyani zinthu zabwino ndi zololedwa zimene Mulungu wakupatsani inu. Ndipo thokozani 16:114 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nahl ⮕ (16:114) ayat 114 in Chichewa

16:114 Surah An-Nahl ayat 114 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 114 - النَّحل - Page - Juz 14

﴿فَكُلُواْ مِمَّا رَزَقَكُمُ ٱللَّهُ حَلَٰلٗا طَيِّبٗا وَٱشۡكُرُواْ نِعۡمَتَ ٱللَّهِ إِن كُنتُمۡ إِيَّاهُ تَعۡبُدُونَ ﴾
[النَّحل: 114]

Motero idyani zinthu zabwino ndi zololedwa zimene Mulungu wakupatsani inu. Ndipo thokozani chisomo cha Mulungu ngati ndiye yekha amene mumapembedza

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فكلوا مما رزقكم الله حلالا طيبا واشكروا نعمة الله إن كنتم إياه, باللغة نيانجا

﴿فكلوا مما رزقكم الله حلالا طيبا واشكروا نعمة الله إن كنتم إياه﴾ [النَّحل: 114]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho idyani zimene Allah wakupatsani zomwe zili zahalali, zabwino; ndipo yamikani mtendere wa Allah ngatidi mukupembedza Iye
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek